Kodi katemera angathandize bwanji kupewa chiwewe cha agalu?

Chiwewe ndi nthenda yowopsa kwambiri m'madera ambiri amu Afilika. Ngakhale zili choncho, ndiyopeweka kudzera mu katemera. Katemera amateteza agalu ndikuwakanikitsa kufalitsa matendawa kwa zinyama zina, inde ngakhalenso kwa anthu.

Detalles Bibliográficos
Autor principal: International Livestock Research Institute
Formato: Video
Lenguaje:ny
Publicado: International Livestock Research Institute 2023
Materias:
Acceso en línea:https://hdl.handle.net/10568/131546
Descripción
Sumario:Chiwewe ndi nthenda yowopsa kwambiri m'madera ambiri amu Afilika. Ngakhale zili choncho, ndiyopeweka kudzera mu katemera. Katemera amateteza agalu ndikuwakanikitsa kufalitsa matendawa kwa zinyama zina, inde ngakhalenso kwa anthu.