Kodi katemera angathandize bwanji kupewa chiwewe cha agalu?
Chiwewe ndi nthenda yowopsa kwambiri m'madera ambiri amu Afilika. Ngakhale zili choncho, ndiyopeweka kudzera mu katemera. Katemera amateteza agalu ndikuwakanikitsa kufalitsa matendawa kwa zinyama zina, inde ngakhalenso kwa anthu.
| Main Author: | |
|---|---|
| Format: | Video |
| Language: | ny |
| Published: |
International Livestock Research Institute
2023
|
| Subjects: | |
| Online Access: | https://hdl.handle.net/10568/131546 |
| Summary: | Chiwewe ndi nthenda yowopsa kwambiri m'madera ambiri amu Afilika. Ngakhale zili choncho, ndiyopeweka kudzera mu katemera. Katemera amateteza agalu ndikuwakanikitsa kufalitsa matendawa kwa zinyama zina, inde ngakhalenso kwa anthu. |
|---|